1 Mbiri 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuyambira kuja ndinaika oweruza ayang'anire anthu anga Israyeli; ndipo ndagonjetsa adani ako onse. Ndikuuzanso kuti Yehova adzakumangira banja.

1 Mbiri 17

1 Mbiri 17:5-14