1 Mbiri 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pokhala Davide m'nyumba mwace, Davideyo anati kwa Natani mneneri, Taona, ndikhala ine m'nyumba yamikungudza, koma Gkasa la cipangano likhala m'nsaru zocinga.

1 Mbiri 17

1 Mbiri 17:1-8