1 Mbiri 16:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nimunene, Tipulumutseni, Mulungu wa cipulumutso cathu;Mutisokolotse ndi kutilanditsa kwa amitundu,Kuti tiyamike dzina lanu loyera,Ndi kudzitamandira naco cilemekezo canu.

1 Mbiri 16

1 Mbiri 16:29-41