1 Mbiri 15:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Sebaniya, ndi Yosafati, ndi Netaneli, ndi Amasai, ndi Zekariya, ndi Benaya, ndi Eliezere, ansembe, analiza malipenga ku likasa la Mulungu; ndi Obedi Edomu ndi Yehiya anali odikira a likasa.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:20-26