1 Mbiri 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anadzimangira nyumba m'mudzi mwace, nakonzeratu malo likasa la Mulungu, naliutsira hema.

1 Mbiri 15

1 Mbiri 15:1-7