1 Mbiri 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Afilisti anamva kuti anamdzoza Davide akhale mfumu ya Aisrayeli onse, Afilisti onse anakwera kufunafuna Davide; ndipo Davide anamva, nawaturukira.

1 Mbiri 14

1 Mbiri 14:2-11