1 Mbiri 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula kunsonga kwa mitengo ya mkandankhuku, pamenepo uturukire kunkhondo; pakuti Mulungu waturukira pamaso pako kukantha gulu la Afilisti.

1 Mbiri 14

1 Mbiri 14:8-17