1 Mbiri 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atafika tsono ku Baala Perazimu, Davide anawakantha komweko; nati Davide, Mulungu anapasula adani anga ndi dzanja langa, ngati pokhamulira madzi. Cifukwa cace analicha dzina la malowo Baala Perazimu.

1 Mbiri 14

1 Mbiri 14:9-17