1 Mbiri 13:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ndi Aisrayeli onse anasewera pamaso pa Mulungu ndi mphamvu yao yonse; ndi nyimbo, ndi azeze, ndi zisakasa, ndi malingaka, ndi nsanje, ndi malipenga,

1 Mbiri 13

1 Mbiri 13:4-13