1 Mbiri 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ndi Aisrayeli onse pamodzi naye anakwera kumka ku Baala, ndiko ku Kiriati-Yearimu wa m'Yuda, kukwera nalo kucokera komweko likasa la Mulungu Yehova wakukhala pa akerubi, kumene aitanirako Dzina.

1 Mbiri 13

1 Mbiri 13:1-7