1 Mbiri 12:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onsewa, ndiwo anthu a nkhondo akusunga malongosoledwe a nkhondo, anadza ku Hebroni ndi mtima wangwiro kudzamlonga Davide mfumu ya Aisraeli onse; ndi onse otsala a Israyeli omwe anali a mtima umodzi kumlonga Davide ufumu.

1 Mbiri 12

1 Mbiri 12:35-40