1 Mbiri 12:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israyeli kuzicita, akuru ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.

1 Mbiri 12

1 Mbiri 12:25-36