1 Mbiri 12:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kuwerenga kwa akuru okonzekeratu kunkhondo, anadzawo kwa Davide ku Hebroni, kupambukitsa ufumu wa Sauli ukhale wace, monga mwa mau a Yehova, ndi: uku.

1 Mbiri 12

1 Mbiri 12:19-29