1 Mbiri 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Davide, Ali yense woyamba kukantha Ayebusi, yemweyo adzakhala mkulu ndi mtsogoleri. Nayamba kukwerako Yoabu mwana wa Zeruya, nakhala mkuru iyeyu.

1 Mbiri 11

1 Mbiri 11:4-12