1 Mbiri 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisai mbale wa Yoabu, ndiye wamkuru wa atatuwa; pakuti anasamulira mazana atatu mkondo wace, nawapha, namveka dzina pakati pa atatuwa.

1 Mbiri 11

1 Mbiri 11:19-26