1 Mbiri 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace anafika Afilisti kubvula za ophedwa, napeza Sauli ndi ana ace adagwa pa phiri la Giliboa.

1 Mbiri 10

1 Mbiri 10:2-14