1 Mbiri 10:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sauli anati kwa wonyamula zida zace, Solola lupanga lako, nundipyoze nalo, angafike osadulidwa awa ndi kundiseka, Koma wonyamula zida zace anakana, popeza anaopa kwambiri. Pomwepo Sauli anatenga lupanga lace, naligwera.

1 Mbiri 10

1 Mbiri 10:1-5