1 Mbiri 1:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namwalira Baalahanani; ndi Hadada anakhala mfumu m'malo mwace; ndipo dzina la mudzi wace ndi Pai; ndi dzina la mkazi wace ndiye Mehetabele mwana wamkazi wa Matradi mwana wamkazi wa Mezahabu.

1 Mbiri 1

1 Mbiri 1:46-54