1 Mbiri 1:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Namwalira Husamu; ndi Hadada mwana wa Bedadi, amene anakantha Midyani ku thengo la Moabu, anakhala mfumu m'malo mwace; ndi dzina la mudzi wace ndi Aviti.

1 Mbiri 1

1 Mbiri 1:41-50