1 Mbiri 1:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mafumu tsono akucita ufumu m'dziko la Edomu, pakalibe mfumu wakucita ufumu pa ana a Israyeli, ndiwo Bela mwana wa Beori; ndi dzina la mudzi wace ndilo Dinaba.

1 Mbiri 1

1 Mbiri 1:36-51