1 Mbiri 1:37-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

37. Ana a Reueli: Nahati, Zera, Sama, ndi Miza.

38. Ndi ana a Seiri: Lotani, ndi Sobala, ndi Zibeoni, ndi Ana, ndi Disoni, ndi Ezeri, ndi Disani.

39. Ndi ana a Lotani: Hori, ndi Homamu; ndipo Timna ndiye mlongo wace wa Lotani.

40. Ana a Sobala: Abiani, ndi Manahati, ndi Ebala, Sefi, ndi Oramu. Ndi ana a Zibeoni: Aiya ndi Ana.

1 Mbiri 1