1 Mbiri 1:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ana a Ketura mkazi wamng'ono wa Abrahamu anabala Zimiramu, ndi Yokisani, ndi Medani, ndi Midyani, ndi Isibaki, ndi Sua. Ndi ana a Yokisani: Seba, ndi Dedani.

1 Mbiri 1

1 Mbiri 1:27-41