1 Mbiri 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Eberi anabala ana amuna awiri, dzina la winayo ndiye Pelegi, popeza masiku ace dziko linagawanika; ndi dzina la mbale wace ndiye Yokitani.

1 Mbiri 1

1 Mbiri 1:17-23