1 Mafumu 9:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu adzayankha, Popeza anasiya Yehova Mulungu wao amene adaturutsa makolo ao m'dziko la Aigupto, natsata milungu yina, nailambira, naitumikira; cifukwa cace Yehova anawagwetsera coipa conseci.

1 Mafumu 9

1 Mafumu 9:5-16