1 Mafumu 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anafika ku Ofiri, natengako golidi matalenti mazana anai mphambu makumi awiri, nafika naye kwa mfumu Solomo.

1 Mafumu 9

1 Mafumu 9:22-28