1 Mafumu 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ameneyo anali akulu a akapitao oyang'anira nchito ya Solomo, mazana asanu mphambu makumi asanu akulamulira anthu ogwira nchito aja.

1 Mafumu 9

1 Mafumu 9:21-28