1 Mafumu 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Farao mfumu ya Aigupto adakwera nalanda Gezeri, nautentha ndi moto, nawapha Akanani akukhala m'mudzimo, naupereka kwaulere kwa mwana wace mkazi wa Solomo.

1 Mafumu 9

1 Mafumu 9:8-17