1 Mafumu 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munalibe kanthu m'likasamo koma magome awiri aja amwala Mose anawalongamo pa Horebu, pamene Yehova anapangana ndi ana a Israyeli, poturuka iwo m'dziko la Aigupto.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:4-12