1 Mafumu 8:58 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti atitembenuzire kwa iye yekha mitima yathu iyende m'njira zace zonse, ndi kusunga malamulo ace onse ndi malemba ace ndi maweruzo ace, amene anawalamulira makolo athu.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:48-66