1 Mafumu 8:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kukhululukira anthu anu adacimwira Inu ndi mphulupulu zao zonse adaparamula nazo kwa Inu; ndipo muwacititsire cifundo iwo amene anawagwira ndende, kuti awacitire cifundo;

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:40-56