1 Mafumu 8:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo akakumbukila mitima yao, ali kudziko kumene anatengedwa ukapolo, nakalapa, nakapembedza inu m'dziko la iwo anawatenga ndende, ndi kuti, Tacimwa, ndipo tacita mphulupulu, tacita moipa;

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:41-51