1 Mafumu 8:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu anu Aisrayeli akawakantha adani ao cifukwa ca kucimwira Inu, ndipo akabweranso kwa Inu, lodi kubvomereza dzina lanu, ndi kupemphera, ndi kupembedza Inu m'nyumba muno;

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:26-36