1 Mafumu 8:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mverani pembedzero la kapolo wanu ndi la anthu anu Aisrayeli, pamene adzapemphera molunjika kumalo kuno; ndipo mverani Inu m'Mwamba mokhala Inumo; ndipo pamene mukumva, khululukirani.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:26-36