1 Mafumu 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova ananena ndi Davide atate wanga, Popeza unafuna m'mtima mwako kumangira dzina langa nyumba, unacita bwino kuti m'mtima mwako unatero.

1 Mafumu 8

1 Mafumu 8:12-25