1 Mafumu 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyumba yace yakukhalamo iye, m'bwalo lina la m'tsogolo mwa khumbilo, linamangidwa cimodzimodzi. Anammangiranso nyumba mwana wamkazi wa Farao, amene adamkwatira Solomo, yofanafana ndi khumbi limeneli.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:6-18