1 Mafumu 7:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi miphikayo, ndi zoolerazo, ndi mbalezo; inde zotengera zonse zimene Hiramu anampangira mfumu Solomo za m'nyumba ya Yehova, zinali za mkuwa wonyezimira.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:38-47