1 Mafumu 7:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mapangidwe a njinga analingana ndi mapangidwe a njinga za gareta, mitanda yace ndi mkombero wace ndi nthiti zace ndi mtima wace zonsezo zinayengedwa.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:27-40