1 Mafumu 7:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga maphaka khumi amkuwa, m'litali mwace mwa phaka limodzi mikono inai, ndi kupingasa kwace mikono inai, ndi msinkhu wace mikono itatu.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:24-32