1 Mafumu 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga mitu iwiri ya mkuwa wosungunula, kulika pamwamba pa nsanamirazo, msinkhu wace wa mutu wina unali mikono isanu, ndi msinkhu wa mutu unzace mikono isanu.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:10-19