1 Mafumu 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo maziko ace anali a miyala ya mtengo wapatali, ndiyo miyala yaikulu, miyala ya mikono khumi, ndi miyala ya mikono isanu ndi itatu.

1 Mafumu 7

1 Mafumu 7:8-20