1 Mafumu 6:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyumbayo pomangidwa inamangidwa ndi miyala yokonzeratu asanaitute; ndipo m'nyumbamo simunamveka: kulira nyundo, kapena nkhwangwa, kapena cipangizo cacitsulo, pomangidwa iyo.

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:1-10