1 Mafumu 6:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitseko ziwiri zomwe zinali za mtengo waazitona, anasemapo ngati akerubi ndi migwalangwa ndi maluwa oti gada, nawakuta ndi golidi; inde anakutanso ndi golidi akerubi ndi migwalangwayo.

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:23-38