1 Mafumu 6:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo phiko limodzi la kerubi linali la mikono isanu, ndi phiko lina la kerubi linalinso la mikono isanu; kuyambira ku nsonga ya phiko limodzi kufikira ku nsonga ya phiko lina inali mikono khumi.

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:21-30