1 Mafumu 6:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyumbayo mfumu Solomo anaimangira Yehova, m'litali mwace munali mikono makumi asanu ndi limodzi, ndi m'mimba mwace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mikono makumi atatu.

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:1-12