1 Mafumu 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'kati mwa nyumba munali mikungudza yosemasema, ngati zikho ndi maluwa oti gada; munali mikungudza yokha yokha simunaoneka mwala ai,

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:14-25