1 Mafumu 6:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadulitsa ndi matabwa amkungudza mikono makumi awiri m'kati mwa nyumba m'tsogolo mwace, kuyambira pansi kulekeza kumitanda; ici anamanga m'katimo cikhale monenera, malo opatulikitsa.

1 Mafumu 6

1 Mafumu 6:12-18