1 Mafumu 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, pamene Hiramu anamva mau ace a Solomo, anakondwera kwakukuru, nati, Alemekezeke Yehova lero amene wampatsa Davide mwana wanzeru akhale mfumu ya anthu aunyinji amenewa.

1 Mafumu 5

1 Mafumu 5:3-12