1 Mafumu 5:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hiramu mfumu ya ku Turo anatuma anyamata ace kwa Solomo, popeza anamva kuti adamdzoza mfumu m'malo mwa atate wace; pakuti Hiramu adakondana ndi Davide masiku onse.

1 Mafumu 5

1 Mafumu 5:1-9