1 Mafumu 4:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ng'ombe zonenepa khumi, ndi ng'ombe za kubusa makumi awiri, ndi nkhosa zana limodzi, osawerenganso ngondo ndi nswala ndi mphoyo ndi mbalame zoweta.

1 Mafumu 4

1 Mafumu 4:15-33