1 Mafumu 4:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo analamulira maiko onse, kuyambira ku Firate kufikira ku dziko la Afilisti ndi ku malire a Aigupto; anthu anabwera nayo mitulo namtumikira Solomo masiku onse a moyo wace.

1 Mafumu 4

1 Mafumu 4:17-27